DPP Yokha Sidzalowanso M’boma: Anamatetule Amenewa Adachezera Kututa Ndalama Ku Sanjika Mpakana Kuthyola Chitseko Atamwalira Bingu-Watero Joyce Banda

JB NDI BINGUMtsogoleri wa dziko lino Joyce Banda wati ndi zokhumudwitsa kwambiri kuti atsogoleri a chipani cha DPP adachezera kututa ndi kuthawitsa ndalama ku nyumba ya chifumu ya Sanjika mpakana kuthyola chitseko nthawi ya maliro a Bingu wa Mutharika.

“Anamatetule amenewa ndi oipa, adathyola chitseko pothawitsa ndalama ndipo mpakana lero chitsekocho sindidachikonzetse kuti udzakhale umboni. Koma ine ndikulumbira kuti ndalama zanga sindizabitsa koma kugwiritsa ntchito moyenera basi. Ndipo lonjezo langa ndi lakuti ineyo sindizakukhumudwitsani.

“Ndipo kaya wina afune kaya asafune, chipani cha DPP chokha sichidzalowanso m’boma,” watero Banda.

Mai banda amayankhula izi ku Chintheche, m’boma la Nkhatabay tsiku Loweluka.

31 Responses to "DPP Yokha Sidzalowanso M’boma: Anamatetule Amenewa Adachezera Kututa Ndalama Ku Sanjika Mpakana Kuthyola Chitseko Atamwalira Bingu-Watero Joyce Banda"

 1. priscilla  July 28, 2013 at 4:46 am

  dpp wil win joYCE whethr u lyk it or nt we are tired with damn tingz

  Reply
 2. nalisero  March 5, 2013 at 1:12 pm

  Sabola wakale sawawa….mukunenayo is history……koma ife timavota on today’s experience and feelings…….DPP idzalamulanso posachedwapa

  Reply
 3. sydney phiri  March 5, 2013 at 11:33 am

  Dokotiwo s. Am’midzi zoona alibe internet but they have relatives in town who have. The suffering they are going through because of Joyce’s policies is unimaginable. The party with real grassroot support is DPP followed by UDF. Am just telling you in advance to save you from blood pressure in 2014.

  Reply
 4. dppnotcomingback?  March 5, 2013 at 4:18 am

  ok?if dpp is not coming bck!joyce bandayo afune asafune peter yekha 2014 boma whether with dpp or not!

  Reply
 5. Ngozi  March 4, 2013 at 9:03 pm

  Joice, you loose mouth will make you fail.Who can vote for mbuli ngati Joice ndi Kachali muli busy kuba chuma cha boma ndikumalalata.Tikudziwa mukuopa DPP. DPP tidzaiike mboma ndi ife basi osati Joice, mbuli yotheratu. Ukhalira yomweyo yokuba ndi ndi kulalataa malawi sadya ndale, wamva???

  Reply
 6. Patriot  March 4, 2013 at 5:56 pm

  Amachita kuthyola manda nkumatulutsa makobiri ankhani nkhani.
  Mbava izi.
  SADZALAMULIRANSO DZIKO LINO AWA.

  Reply
 7. northerner  March 4, 2013 at 3:19 pm

  Peter and DPP will continue to be a thorn to bakha JB even beyond 2014 because DPP will be in Govt or will be the leader of oposition(if PP will rig) with majority MPs. PP ikhaulenge. We are tired of being ruled by IMF and Europe through this stupid pupet joice banda.

  Reply
 8. Ngozi  March 4, 2013 at 2:26 pm

  Joice what you have to know is that you are very stupid and satanic.We know you were hungery for leadership, alipo umagonanaye ku DPP ndichifukwa umataya nthawi kukamba za DPP.Olo unene zatani ife sitidzakuvotera ndipo anthu atopa ndi ulamulilo opanda tsogolo upite kun Korea komweko ukawathandize za chuma.Ndale sutha koma nkhanza basi.Timavota ndiife ndipo ukutaya nthawi kukamba za DPP tiwonana 2014, bola ufike.Ulembanso ina kalata

  Reply
 9. Cheyo the real northerner  March 4, 2013 at 1:53 pm

  Ndiye mwatani ngati head of govt machinery. Zinachitika m april last year ndiye all this time where were you. Cheap politics no room in malawi.

  Reply
 10. Legson Mtunga  March 3, 2013 at 6:58 pm

  Maiwo akutero akuti koma UDF

  Reply
 11. Hilda dzina la Hule  March 3, 2013 at 5:12 pm

  dokotiwo S shupit zako. Ukuyesa mmizi ndiye manyi ako a JBwo akuwafuna ndani. Azingokoketsa mapilikanilo achewo kwa amuna!

  Reply
 12. kachepa mkayenda  March 3, 2013 at 1:53 pm

  aaah zaziii! Chule

  Reply
 13. dada  March 3, 2013 at 1:11 pm

  Ngati mukuchitachi ndi chipongwe muonanso mulephera chisankho

  Reply
 14. Chebomani  March 3, 2013 at 12:49 pm

  Kodi Joyce ku Sanjika walowako liti kuti uzikanena za chitseko chosweka lero? Iyeyu ndiye mbava nambala wani. Pamene amalowa m’boma anali ndi K24,000 ku account yake pano ku account yomweyo kuli K36 billion kwacha. Kuba kupose apa? Komanso bola kuba kusiyana ndi uhule amachita Joyce wolanda nkhalamba ija yotchedwa Richard Banda. President amakhala wolanda amuna. Kodi iyeyu Joice ku Sanjika amapitako nthawi imene ija kuti akadziwe za kumeneko? Iye woyera ngati mngelo akuopa chani kuti apange declare ma assets ake?

  Reply
 15. Tonde  March 3, 2013 at 7:24 am

  Aaaaa mwanamatu apa. Kodi anavotera PP ndani? Mwalowa kuzera ku mortuary. Pp sinawinepo masankho bolanso Dpp inakwapula. Kwathu chipani chanucho cha Poverty Promotion kulibe.

  Reply
 16. BINGULA  March 3, 2013 at 6:49 am

  Zopusa basi you think ukuchitazo akukondwa nazo ndi ndani, they are those amene akudya nawetu, mmene tikuvutikiramu ndizikayima pamzere kumavotera iweyo. And amzakowo ndiokuba why then are you denying to declare your assets to prove your innocence, prove to Malawi that u indeed a God fearing leader and u want to lead by example, ine voti yanga sudzaiona my relations enclussive. From today stop castigating okuba amzako, coz u are one of them, aliyense can steal when he or she is in the hot seat, that should not be a campaign tool. Mind u we are just waiting for the government of God which will never be like this.

  Reply
 17. khalibudu  March 3, 2013 at 4:53 am

  pitala sawina kumene

  Reply
 18. Mambucha  March 3, 2013 at 4:52 am

  JB does not know what she is taking about!

  Reply
 19. Hello  March 3, 2013 at 1:41 am

  I thought she is there because of being DPP voted into Govt? It is DPP in government right now, check the faces who wer campaining on DPP ticket and who is in government right now. They just forgtot D on the PP anyway. Same faces more serious blunders… May be it should be said no more party in govt with PP on their pary name.

  Reply
 20. Chidambo  March 2, 2013 at 9:20 pm

  Mumangeni ngati mukunena zowona. Ife si tikukufunani, tikufuna iyeyu. Ndinu oipa. Please osawononga zitseko kumeneko.

  Reply
 21. Mic kokota  March 2, 2013 at 9:03 pm

  Ndiye aulure za chuma chake.

  Reply
 22. daph walker  March 2, 2013 at 8:40 pm

  Inu ndiye simudzalowa kumango yamikira zamasiyezi basi-kwatha

  Reply
 23. Chepapwicheh  March 2, 2013 at 8:40 pm

  achitsilu mai wa j banda,nanga bwanji ukukana kunena za chuma chako? hule iwe.

  Reply
 24. becks  March 2, 2013 at 8:37 pm

  Ukunama joice

  Reply
 25. daph walker  March 2, 2013 at 8:30 pm

  Mabodza sayendetsa boma koma nzeru. Mukunena mabodza chilowele upule koma zikukukanikani.

  Reply
 26. Five Moba  March 2, 2013 at 8:21 pm

  She talking rubish, thats cheap politics, imeneyo ndikampeni, kodi ukuwona ngati ana ukuwauza zimenezo? Akudziwa zowona zake, cheap propergander, panyelo pako, wolephela iwe, khak care taker

  Reply
 27. Richard yr Sweetiee  March 2, 2013 at 7:47 pm

  khawuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuu JB samala ndi ma speach ako ungazikole wekha,,,,,, akuvotera ndi makutu akowo yanga yokha vote ng’oooooooooooooooo APM basi

  Reply
 28. bt  March 2, 2013 at 7:42 pm

  opinion poll ukuona?ngati ukuyesa uwina ungozinamiza chabe.anthu atopa nawe.

  Reply
 29. skopion  March 2, 2013 at 7:24 pm

  zau hule basi!

  Reply
 30. Bonya  March 2, 2013 at 7:22 pm

  Manyi a pulezident ngati JB sindinaonenso. Bwanji uli ndi 19% yokha pomwe Peter is close to 60%. Maujeni ako achikazi!

  Reply
  • dokotiwo S  March 3, 2013 at 4:40 am

   Shupiti unamva kuti amu midzi ali ndi internet.munatibela agalu inu a dphi phi

   Reply

Leave Comments Here