spot_img
Saturday, January 11, 2025
spot_img
HomeLatestMsonda wapepesa kwa a Mutharika: "Pepani a Dadie mundikhululikire ndachimina"

Msonda wapepesa kwa a Mutharika: “Pepani a Dadie mundikhululikire ndachimina”

Membala wa Komiti yaikulu ya chipani cha DPP a Ken Nsonda apepetsa kwa mtsogoleri wachipachi a Peter Mutharika pazomwe wakhala akuchita munthawi yambuyoyi zonyoza iwo komanso chipanichi.

Izi zikutsira kudzudzulidwa pagulu ndi mtsogoleri wachipanichi kaamba ka makhalidwe ake omwe Mutharika akuti ndiobweletsa mpungwepungwe.

Mutharika moonetsa kukwiya anaudza Nsonda kuti: “Ngati mukuona kuti simulemekedza utsogoleri wachipani ndibwino mutuluke DPP.”

Koma Nsonda wanenetsa kuti alipambuyo pa Mutharika ndipo wamupempha mtsogoleri-yu kuti ayimenso pachisankho.

Pakadali pano, a Mutharika alengeza kuti iwo adzapikitsana nawo pamsonkhano waukulu omwe uzachitike pa 26 komanso 27 m’boma la Mangochi.

Mawu awo a Mutharika ati akufuna kuti adzatsogolere chipani cha DPP muchaka cha 2025 kuti chipanichi chizabwelere m’boma. Kulengeza kwa Mutharika kukudza pomwe wachiwiri kwamtsogoleri wakale wachipanichi kuchigawo chakumwera Kondwani Nankhumwa analengezanso zopikitsana nawo paudindow

RELATED ARTICLES

LEAVE A REPLY

Please enter your comment!
Please enter your name here

- Advertisment -

Most Popular