spot_img
Saturday, January 4, 2025
spot_img
HomeLatestDear Chilima, Chakwera will never love you more than APM

Dear Chilima, Chakwera will never love you more than APM

By Bashir Al Bashir

“Koma tinagwirizana kuti ndikamaliza ma term awiri, Chilima adzakhala President,” said Professor Peter Mutharika in 2022.

Mgwirizano opanda mboni, opanda kusainirana, koma the gentleman in APM couldn’t betray Chilima on what they agreed kumbali, he accepted publicly.

“Palibe mgwirizano oterewo,” Chakwera, 2021 kukana mgwirizano osayinirana pagulu, amipingo mbalimu, kuwukana pagulu.

Ndikanakhala SKC, panopa, wina yapakamwa koma amavomera kugulu, wina yosainirana pagulu koma amayikana, zoti Mkaka anali jijirijijiri kuperekera mapepala osainirana koma anakana mmaso muli gwaa kuti sakudziwa kanthu, awo sianthu.

Bwana pitani kwa APM, somehow, in all fairness, Dr. Chilima anayankhula zambiri against APM, koma palibe olo tsiku limodzi APM anamubwezera Chilima, that’s unshakable love APM has for SKC, akanatha kumpezera mulandu monga anachitira Chakwera, APM sanapange, father’s love, ana timaphophonya pena, bambo amamvetsetsa

Only man who loved and loves SKC among the two remains APM, chetee wa APM kunali kuwonelera mwana afika nazo pati, wakanika, bambo wadzuka kupulumutsa dziko mkamwa mwa ng’ona ndi mwana yemwe. SKC go back and support APM in 2025, you lose nothing Bwana nthawi iripo yambiri

Munthu umakhala komwe kuli chikondi, nkwabwino kugonera therere pamtendere kulekana ndi nyama vilombo vikukutambira daily, mishaps happened, but chakwera will never love you more than APM.

RELATED ARTICLES

1 COMMENT

LEAVE A REPLY

Please enter your comment!
Please enter your name here

- Advertisment -

Most Popular