spot_img
Tuesday, January 28, 2025
spot_img
HomeLatestZAULULIKA: KU DOWA KULI MA AREA A CHINYENGO OPANGIDWA NDI CHIPANI CHA...

ZAULULIKA: KU DOWA KULI MA AREA A CHINYENGO OPANGIDWA NDI CHIPANI CHA MCP

Pamene zisankho za chipulura zayandikira, ku Chipani cha Kongeresi, pali mphekesera zakuti ma Area a chinyengo akanidwa ndi akuluakulu oyang’anira Chigawo chapakati.

Malingana ndi Shadow MP waku Bowe, Lydia ndi JB Chafukira yemwe anali nawo pakati pa Ma Shadow ku ofesi ya Chilondora, watitsina khutu kuti zinali zodabwitsa kuona ma area okwana 497 akulamulidwa ndi Constituency Chairman, Chapuma.

Naye m’modzi mwa executive komiti ya Chigawo chapakati, Willard Gwengwe anali odabwitsika ndi kuchuluka kwa ma Area.

Mu chaka cha 2018 ma Area analipo okwana 245 okha basi.

Pali mphekesera zosonyeza kuti ma Area ena anaonjezeleka ndi mkulu wina yemwenso akuyima nawo ku Dowa Ngala.

Kuderali kuli ma Shadow okwana 12.

Zikuonetsa ngati mnyamata yemwe dzina lake ndi Henry Msonkho Phiri ndiye watekesa ku Dowa Ngala.

RELATED ARTICLES

LEAVE A REPLY

Please enter your comment!
Please enter your name here

- Advertisment -

Most Popular