spot_img
Saturday, February 15, 2025
spot_img
HomeLatestNtchito zamanja anga zikundichitira umboni, Watero Chakwera

Ntchito zamanja anga zikundichitira umboni, Watero Chakwera

Powomba mkota pantchito zosiyanasiyana zachitukuko zomwe zachitika m’maboma onse adziko lino pansi pa utsogoleri wawo, Dr Lazarus Chakwera ati aMalawi adzionera okha kuti utsogoleri wawo ndiomangilira dziko lonse monga mtundu umodzi wa aMalawi.

Iwo ati ntchito zamanja awo zikuwachitira umboni ndipo akuyang’ana chitsogolo kuti chitukukochi chipitilire mdziko muno.

Pakadali pano mtsogoleri wadziko linoyu akutuluka m’Nyumba ya Malamulo.

Sipikala wa Nyumba ya Malamulo a Catherine Gotani Hara atseka nyumbayi ndipo aphungu adzakumana Lolemba pa 17 February 2025 kudzapitiriza zokambirana zawo.

RELATED ARTICLES

LEAVE A REPLY

Please enter your comment!
Please enter your name here

- Advertisment -

Most Popular